1 Mbiri 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Afilisiti anasiya milungu yawo kumeneko ndipo Davide atalamula, milunguyo anaitentha pamoto.+