1 Mbiri 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Patapita nthawi, Afilisiti aja anabweranso nʼkuyamba kuukira anthu okhala mʼchigwacho.+