1 Mbiri 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za bakazo, ukatuluke nʼkuyamba kumenyana nawo chifukwa Mulungu woona adzakhala atatsogola kukapha asilikali a Afilisiti.”+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:15 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, tsa. 21
15 Ndiyeno ukakamva phokoso la kuguba pamwamba pa zitsamba za bakazo, ukatuluke nʼkuyamba kumenyana nawo chifukwa Mulungu woona adzakhala atatsogola kukapha asilikali a Afilisiti.”+