1 Mbiri 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kumanga nyumba zake mu Mzinda wa Davide ndipo anakonza malo oikapo Likasa la Mulungu woona, nʼkulimangira tenti.+
15 Davide anapitiriza kumanga nyumba zake mu Mzinda wa Davide ndipo anakonza malo oikapo Likasa la Mulungu woona, nʼkulimangira tenti.+