1 Mbiri 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawi imeneyi mʼpamene Davide ananena kuti: “Alevi okha ndi amene ayenera kunyamula Likasa la Mulungu woona, chifukwa Yehova anasankha iwowa kuti azinyamula Likasa la Yehova ndiponso azimutumikira nthawi zonse.”+
2 Pa nthawi imeneyi mʼpamene Davide ananena kuti: “Alevi okha ndi amene ayenera kunyamula Likasa la Mulungu woona, chifukwa Yehova anasankha iwowa kuti azinyamula Likasa la Yehova ndiponso azimutumikira nthawi zonse.”+