1 Mbiri 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Davide anasonkhanitsa Aisiraeli onse ku Yerusalemu kuti akanyamule Likasa la Yehova, kupita nalo kumalo amene iye anakonza kuti akaliike.+
3 Ndiyeno Davide anasonkhanitsa Aisiraeli onse ku Yerusalemu kuti akanyamule Likasa la Yehova, kupita nalo kumalo amene iye anakonza kuti akaliike.+