1 Mbiri 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuchokera ku banja la Merari, panali Asaya+ mtsogoleri wawo ndi abale ake okwana 220.