1 Mbiri 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuchokera ku banja la Gerisomu, panali Yoweli+ mtsogoleri wawo ndi abale ake okwana 130.