1 Mbiri 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kuchokera pa mbadwa za Elizafana,+ panali Semaya mtsogoleri wawo ndi abale ake okwana 200.