1 Mbiri 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuchokera pa mbadwa za Uziyeli,+ panali Aminadabu mtsogoleri wawo ndi abale ake okwana 112.