1 Mbiri 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso Davide anaitanitsa Zadoki+ ndi Abiyatara,+ omwe anali ansembe. Anaitanitsanso Alevi awa: Uriyeli, Asaya, Yoweli, Semaya, Elieli ndi Aminadabu.
11 Komanso Davide anaitanitsa Zadoki+ ndi Abiyatara,+ omwe anali ansembe. Anaitanitsanso Alevi awa: Uriyeli, Asaya, Yoweli, Semaya, Elieli ndi Aminadabu.