1 Mbiri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Alevi anakanyamula Likasa la Mulungu woona pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo,+ mogwirizana ndi zimene Mose anawalamula potsatira mawu a Yehova.
15 Ndiyeno Alevi anakanyamula Likasa la Mulungu woona pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo,+ mogwirizana ndi zimene Mose anawalamula potsatira mawu a Yehova.