1 Mbiri 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Aleviwo anasankha Hemani+ mwana wa Yoweli. Pa abale ake, anasankhapo Asafu+ mwana wa Berekiya ndipo pa abale awo a kubanja la Merari, anasankhapo Etani+ mwana wa Kusaya.
17 Choncho Aleviwo anasankha Hemani+ mwana wa Yoweli. Pa abale ake, anasankhapo Asafu+ mwana wa Berekiya ndipo pa abale awo a kubanja la Merari, anasankhapo Etani+ mwana wa Kusaya.