1 Mbiri 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Hemani,+ Asafu+ ndi Etani anawasankha kuti aziimba ndi zinganga zakopa.*+