1 Mbiri 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sebaniya, Yosafati, Netaneli, Amasai, Zekariya, Benaya ndi Eliezere, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga mokweza patsogolo pa Likasa la Mulungu woona.+ Obedi-edomu ndi Yehiya nawonso anali alonda apageti panyumba yomwe munkakhala Likasa.
24 Sebaniya, Yosafati, Netaneli, Amasai, Zekariya, Benaya ndi Eliezere, omwe anali ansembe, ankaimba malipenga mokweza patsogolo pa Likasa la Mulungu woona.+ Obedi-edomu ndi Yehiya nawonso anali alonda apageti panyumba yomwe munkakhala Likasa.