1 Mbiri 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Davide ndi akulu a Isiraeli ndiponso atsogoleri a anthu 1,000 ankayenda mosangalala+ limodzi ndi likasa la pangano la Yehova kuchokera kunyumba kwa Obedi-edomu.+
25 Davide ndi akulu a Isiraeli ndiponso atsogoleri a anthu 1,000 ankayenda mosangalala+ limodzi ndi likasa la pangano la Yehova kuchokera kunyumba kwa Obedi-edomu.+