1 Mbiri 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mulungu woona atathandiza Alevi omwe ananyamula likasa la pangano la Yehova, iwo anapereka nsembe ngʼombe zazingʼono zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.+
26 Mulungu woona atathandiza Alevi omwe ananyamula likasa la pangano la Yehova, iwo anapereka nsembe ngʼombe zazingʼono zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.+