1 Mbiri 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Davide, Alevi onse onyamula Likasa, oimba ndiponso Kenaniya amene ankayangʼanira oimba komanso ntchito yonyamula Likasa, anavala mikanjo yodula manja, yansalu yabwino kwambiri. Koma Davide anavalanso efodi wansalu.+
27 Davide, Alevi onse onyamula Likasa, oimba ndiponso Kenaniya amene ankayangʼanira oimba komanso ntchito yonyamula Likasa, anavala mikanjo yodula manja, yansalu yabwino kwambiri. Koma Davide anavalanso efodi wansalu.+