1 Mbiri 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aisiraeli onse ankapita limodzi ndi likasa la pangano la Yehova akufuula mokondwera+ ndiponso akuliza nyanga za nkhosa ndi malipenga.+ Iwo ankaimbanso mokweza zinganga, zoimbira za zingwe ndi azeze.+
28 Aisiraeli onse ankapita limodzi ndi likasa la pangano la Yehova akufuula mokondwera+ ndiponso akuliza nyanga za nkhosa ndi malipenga.+ Iwo ankaimbanso mokweza zinganga, zoimbira za zingwe ndi azeze.+