1 Mbiri 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma likasa la pangano la Yehova litafika mu Mzinda wa Davide,+ Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anasuzumira pawindo ndipo anaona Mfumu Davide akudumphadumpha ndi kusangalala. Ndiyeno Mikala anayamba kumunyoza mumtima mwake.+
29 Koma likasa la pangano la Yehova litafika mu Mzinda wa Davide,+ Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anasuzumira pawindo ndipo anaona Mfumu Davide akudumphadumpha ndi kusangalala. Ndiyeno Mikala anayamba kumunyoza mumtima mwake.+