1 Mbiri 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtsogoleri wawo anali Asafu,+ wachiwiri wake anali Zekariya. Ndipo Yeyeli, Semiramoti, Yehiela, Matitiya, Eliyabu, Benaya, Obedi-edomu ndi Yeyeli+ ankaimba ndi zoimbira za zingwe ndiponso azeze.+ Asafu ankaimba zinganga.+
5 Mtsogoleri wawo anali Asafu,+ wachiwiri wake anali Zekariya. Ndipo Yeyeli, Semiramoti, Yehiela, Matitiya, Eliyabu, Benaya, Obedi-edomu ndi Yeyeli+ ankaimba ndi zoimbira za zingwe ndiponso azeze.+ Asafu ankaimba zinganga.+