1 Mbiri 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nyadirani dzina lake loyera.+ Mitima ya anthu ofunafuna Yehova isangalale.+