1 Mbiri 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Funafunani Yehova+ ndipo muzidalira mphamvu zake. Nthawi zonse muzimupempha kuti akuthandizeni.*+