1 Mbiri 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Dziko lonse lapansi liimbire Yehova! Tsiku ndi tsiku muzilengeza za chipulumutso chake!+