1 Mbiri 16:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anawasiya kuti azipereka nsembe zopsereza kwa Yehova nthawi zonse paguwa lansembe zopsereza, mʼmawa ndi madzulo, mogwirizana ndi zonse zolembedwa mʼChilamulo cha Yehova chimene analamula Aisiraeli.+
40 Anawasiya kuti azipereka nsembe zopsereza kwa Yehova nthawi zonse paguwa lansembe zopsereza, mʼmawa ndi madzulo, mogwirizana ndi zonse zolembedwa mʼChilamulo cha Yehova chimene analamula Aisiraeli.+