1 Mbiri 16:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani ndi Yedutuni+ ndiponso amuna onse amene anawasankha mochita kuwatchula mayina kuti azithokoza Yehova,+ chifukwa “chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.”+
41 Iwowa anali limodzi ndi Hemani ndi Yedutuni+ ndiponso amuna onse amene anawasankha mochita kuwatchula mayina kuti azithokoza Yehova,+ chifukwa “chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.”+