1 Mbiri 16:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Hemani+ ndi Yedutuni anawasiya kuti aziimba malipenga, zinganga ndi zipangizo zina zimene ankagwiritsa ntchito potamanda Mulungu woona* ndipo ana a Yedutuni+ anali alonda apageti.
42 Hemani+ ndi Yedutuni anawasiya kuti aziimba malipenga, zinganga ndi zipangizo zina zimene ankagwiritsa ntchito potamanda Mulungu woona* ndipo ana a Yedutuni+ anali alonda apageti.