1 Mbiri 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pita ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Si iweyo amene udzandimangire nyumba yoti ndizikhalamo.+
4 “Pita ukauze mtumiki wanga Davide kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Si iweyo amene udzandimangire nyumba yoti ndizikhalamo.+