1 Mbiri 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa Aisiraeli mpaka lero, sindinakhalepo mʼnyumba koma nthawi zonse ndinkayendayenda kuchoka mutenti kupita mutenti ndiponso kuchoka muchihema chopatulika kupita muchihema china.*+
5 Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa Aisiraeli mpaka lero, sindinakhalepo mʼnyumba koma nthawi zonse ndinkayendayenda kuchoka mutenti kupita mutenti ndiponso kuchoka muchihema chopatulika kupita muchihema china.*+