1 Mbiri 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa kumene unkaweta nkhosa kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+
7 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa kumene unkaweta nkhosa kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Aisiraeli.+