1 Mbiri 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndidzakhala nawe kulikonse kumene ungapite+ ndipo ndidzagonjetsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzachititsa kuti dzina lako lidziwike ngati mmene zimakhalira ndi anthu otchuka mʼdzikoli.+
8 Ine ndidzakhala nawe kulikonse kumene ungapite+ ndipo ndidzagonjetsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzachititsa kuti dzina lako lidziwike ngati mmene zimakhalira ndi anthu otchuka mʼdzikoli.+