1 Mbiri 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 pa nthawi imene ndinasankha oweruza kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli.+ Ndipo ndidzagonjetsa adani ako onse.+ Kuwonjezera pamenepo, ndikukuuza kuti: ‘Yehova adzakumangira nyumba.’*
10 pa nthawi imene ndinasankha oweruza kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli.+ Ndipo ndidzagonjetsa adani ako onse.+ Kuwonjezera pamenepo, ndikukuuza kuti: ‘Yehova adzakumangira nyumba.’*