1 Mbiri 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Sindidzamuchotsera chikondi changa chokhulupirika+ ngati mmene ndinachitira kwa munthu yemwe analipo iwe usanakhalepo.+
13 Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Sindidzamuchotsera chikondi changa chokhulupirika+ ngati mmene ndinachitira kwa munthu yemwe analipo iwe usanakhalepo.+