1 Mbiri 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Mulungu, kuwonjezeranso pamenepa mwandiuza kuti nyumba ya ine mtumiki wanu idzakhazikika mpaka mʼtsogolo kwambiri+ ndipo inu Yehova Mulungu, mwanditenga ine ngati munthu woyenera kukwezedwa.*
17 Inu Mulungu, kuwonjezeranso pamenepa mwandiuza kuti nyumba ya ine mtumiki wanu idzakhazikika mpaka mʼtsogolo kwambiri+ ndipo inu Yehova Mulungu, mwanditenga ine ngati munthu woyenera kukwezedwa.*