1 Mbiri 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu Yehova, chifukwa cha ine mtumiki wanu, komanso mogwirizana ndi zofuna za mtima wanu,* mwachita zazikulu zonsezi pondidziwitsa kuti mumachita zazikulu.+
19 Inu Yehova, chifukwa cha ine mtumiki wanu, komanso mogwirizana ndi zofuna za mtima wanu,* mwachita zazikulu zonsezi pondidziwitsa kuti mumachita zazikulu.+