1 Mbiri 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dzina lanu likhalepobe ndipo likwezeke+ mpaka kalekale kuti anthu anene kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi Mulungu wa Isiraeli.’ Ndipo nyumba ya ine mtumiki wanu Davide ikhazikike pamaso panu.+
24 Dzina lanu likhalepobe ndipo likwezeke+ mpaka kalekale kuti anthu anene kuti, ‘Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi Mulungu wa Isiraeli.’ Ndipo nyumba ya ine mtumiki wanu Davide ikhazikike pamaso panu.+