1 Mbiri 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide analanda Hadadezeri magaleta 1,000 komanso anagwira amuna 7,000 okwera pamahatchi ndi asilikali 20,000 oyenda pansi.+ Kenako Davide anapundula* mahatchi onse a magaleta nʼkungosiya mahatchi 100.+
4 Davide analanda Hadadezeri magaleta 1,000 komanso anagwira amuna 7,000 okwera pamahatchi ndi asilikali 20,000 oyenda pansi.+ Kenako Davide anapundula* mahatchi onse a magaleta nʼkungosiya mahatchi 100.+