1 Mbiri 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso Davide anatenga kopa* wambiri ku Tibati ndi ku Kuni, mizinda ya Hadadezeri. Solomo anagwiritsa ntchito kopa ameneyu kupangira thanki yosungira madzi,+ zipilala ndi ziwiya zina.+
8 Komanso Davide anatenga kopa* wambiri ku Tibati ndi ku Kuni, mizinda ya Hadadezeri. Solomo anagwiritsa ntchito kopa ameneyu kupangira thanki yosungira madzi,+ zipilala ndi ziwiya zina.+