-
1 Mbiri 18:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 nthawi yomweyo anatumiza mwana wake Hadoramu kwa Mfumu Davide kukamufunsa za moyo wake ndiponso kukamuyamikira chifukwa chomenyana ndi Hadadezeri nʼkumugonjetsa. (Chifukwa Hadadezeri ankakonda kumenyana ndi Toi.) Popita kwa Davide, Hadoramu anatenga zinthu zasiliva, zagolide ndi zakopa.
-