1 Mbiri 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu Davide anapereka zinthu zimenezi kwa Yehova+ pamodzi ndi siliva komanso golide amene anatenga kuchokera ku mitundu yonse. Anatenga kuchokera kwa Aedomu, Amowabu, Aamoni,+ Afilisiti+ ndi Aamaleki.+
11 Mfumu Davide anapereka zinthu zimenezi kwa Yehova+ pamodzi ndi siliva komanso golide amene anatenga kuchokera ku mitundu yonse. Anatenga kuchokera kwa Aedomu, Amowabu, Aamoni,+ Afilisiti+ ndi Aamaleki.+