1 Mbiri 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anakhazikitsa midzi ya asilikali ku Edomu ndipo Aedomu onse anakhala antchito a Davide.+ Yehova ankathandiza Davide kuti apambane kulikonse kumene wapita.+
13 Iye anakhazikitsa midzi ya asilikali ku Edomu ndipo Aedomu onse anakhala antchito a Davide.+ Yehova ankathandiza Davide kuti apambane kulikonse kumene wapita.+