1 Mbiri 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Benaya mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti+ ndipo ana aamuna a Davide anali achiwiri kwa mfumu.
17 Benaya mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti+ ndipo ana aamuna a Davide anali achiwiri kwa mfumu.