-
1 Mbiri 19:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Zitatero, Davide anati: “Ndimusonyeza Hanuni mwana wa Nahasi chikondi chokhulupirika+ chifukwa bambo ake anandisonyeza chikondi chokhulupirika.” Choncho Davide anatumiza anthu kuti akamutonthoze chifukwa cha imfa ya bambo ake. Koma atumiki a Davidewo atafika mʼdziko la Aamoni+ kuti atonthoze Hanuni,
-