1 Mbiri 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno anamuuza kuti: “Ukaona kuti Asiriya+ akundigonjetsa, ubwere udzandipulumutse. Koma Aamoni akayamba kukugonjetsa, ineyo ndibwera kudzakupulumutsa.
12 Ndiyeno anamuuza kuti: “Ukaona kuti Asiriya+ akundigonjetsa, ubwere udzandipulumutse. Koma Aamoni akayamba kukugonjetsa, ineyo ndibwera kudzakupulumutsa.