-
1 Mbiri 19:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma Asiriya anayamba kuthawa Aisiraeli ndipo Davide anapha asilikali a Asiriya 7,000 okwera magaleta komanso asilikali 40,000 oyenda pansi. Iye anaphanso Sofaki, mkulu wa gulu lankhondo la Asiriya.
-