1 Mbiri 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti, ndipo Elihanani mwana wa Yairi anapha Lami, mchimwene wake wa Goliyati+ wa ku Gati, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu.+
5 Kenako panabukanso nkhondo ina ndi Afilisiti, ndipo Elihanani mwana wa Yairi anapha Lami, mchimwene wake wa Goliyati+ wa ku Gati, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu.+