-
1 Mbiri 21:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma Yowabu anati: “Yehova awonjezere anthu ake kuwirikiza ka 100. Mbuyanga mfumu, kodi anthu onsewa si anu komanso si atumiki anu kale? Ndiye nʼchifukwa chiyani mbuyanga mukufuna kuchita zimenezi? Nʼchifukwa chiyani mukufuna kupalamulitsa Aisiraeli?”
-