1 Mbiri 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Davide atamva zimenezo, anauza Gadi kuti: “Zimenezi zikundisowetsa mtendere kwambiri. Kuli bwino ndilangidwe ndi Yehova, chifukwa chifundo chake nʼchachikulu,+ koma ndisalangidwe ndi munthu.”+
13 Davide atamva zimenezo, anauza Gadi kuti: “Zimenezi zikundisowetsa mtendere kwambiri. Kuli bwino ndilangidwe ndi Yehova, chifukwa chifundo chake nʼchachikulu,+ koma ndisalangidwe ndi munthu.”+