1 Mbiri 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno mngelo wa Yehova anauza Gadi+ kuti auze Davide kuti apite kumalo opunthira mbewu a Orinani wa Chiyebusi, nʼkukamangira Yehova guwa lansembe.+
18 Ndiyeno mngelo wa Yehova anauza Gadi+ kuti auze Davide kuti apite kumalo opunthira mbewu a Orinani wa Chiyebusi, nʼkukamangira Yehova guwa lansembe.+