1 Mbiri 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Davide anapatsa Orinani ndalama zokwana masekeli* 600 agolide zogulira malowo.